Lero tili ku Lirangwe ndi King’s Choice Salt Road Show!
Monga momwe timachitilira, tabweretsanso ndi mphoto zosiyanasiyana pamene anthu
akupikisana ndi kusangalala. Ndipo King’s Choice Road Show ikubwelera kudera kwanu posachedwa!
King’s Choice ndi mchere wopatsa thanzi, wokoma, komanso wosaboola m’thumba! Kaguleni wanu lero.

Not any Videos.

BESbswy